Malinga Bill Yanga Prod by DJ Sley

Lyrics.

yoh yoh yoh yeah
mmmmh mmmmh
Yachina
yeah yeah

Undipeza pa home ground san silo
Ubweletse ganja aise five kilo
Ndima liva soft life five pillows
Maluzi kuno nde tikuwachinya five zero

Mfana olimbikila hustle ngati maskini
Pakhomo zingati aise? five pini
Mafana kuyesa ngati mwina ndima user khini
Ma babe ndungogwila ma bomba Charles Swini

Kuspenda money ngati mwana wa politician
money laugh haha ndikugiligishani
Phone yanga osaimba palibepo mission
Iye nde dancehall ina ija tiku deletitsani

Oii ndili bwino muli bwa?
Tikumwela kuno inu muli kwa?
Pa bwandilo tinapitilapo nyama
Zakathela short time ndi bwa?

Pasapezeke fanta pa bill yanga
No iyi si bill yanga
Ndavala tinted ayesa Steve Wonder
Mowa wina ukutanipo pa bill yanga
Bartender noo iyi si bill yanga
Noo iyi si bill yanga
Mkazi uyo yekha amwa pa bill yanga
Ana akenso adzakhala pa will yanga

Ma style ambiri mbiri
Hot like piri piri
Two two three three
Black beema
Kukumveka dancehall ko ndikomwe ife tili
ndine chair wa zinginizi who? Bakili kili

Genna wa droppa ina
Ona zima Babe zikuvina
Pa Bill yanga vunga nso round ina
Amafuna abele style ndasintha kuika ina

Ndakumana ndichichi mwana Phuli Phuli
Chondipatsa nkhuli nkhuli
Chimafila dancehall ndichipatsa phuli phuli
Rich like Muli Muli
Muli bwa? muli uli?
Weh we deh yachina hehehe fully fully

Ukandipeza pa Zode (Tsaa)
Ndili ndi achina Mode (Staar)
Amafuna glass ndampatsa ya Gin
I didn’t know kuti amafuna aphode

Pasapezeke fanta pa bill yanga
No iyi si bill yanga
Ndavala tinted ayesa Steve Wonder
Mowa wina ukutanipo pa bill yanga
Bartender noo iyi si bill yanga
Noo iyi si bill yanga
Mkazi uyo yekha amwa pa bill yanga
Ana akenso adzakhala pa will yanga

Pasapezeke fanta pa bill yanga
No iyi si bill yanga
Ndavala tinted ayesa Steve Wonder
Mowa wina ukutanipo pa bill yanga
Bartender noo iyi si bill yanga
Noo iyi si bill yanga
Mkazi uyo yekha amwa pa bill yanga
Ana akenso adzakhala pa will yanga

Yeah Yeah
Yachina, Fully!
You know how di ting go my G
Weh we deh

Ife ndi mafumu like Makanjira
Ku spenda money Mpinganjira
Ndikafika likkle bwoy sintha njira
Big dawg yow puppy bwoy pinda nchila
weh we deh

Loading

Share

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *